Ekisodo 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano, tamvera. Ndikutuma kwa Farao kuti ukatulutse anthu anga ana a Isiraeli ku Iguputo.”+ Ekisodo 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako Mose ndi Aroni anapita kwa Farao ndi kumuuza kuti:+ “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Lolani anthu anga apite m’chipululu kuti akachite chikondwerero.’”+
5 Kenako Mose ndi Aroni anapita kwa Farao ndi kumuuza kuti:+ “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Lolani anthu anga apite m’chipululu kuti akachite chikondwerero.’”+