1 Samueli 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Samueli anauza anthuwo kuti: “Yehova ndiye mboni, iye amene anagwiritsa ntchito Mose ndi Aroni, amenenso anatulutsa makolo anu m’dziko la Iguputo.+ Salimo 105:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiyeno anatumiza Mose mtumiki wake,+Ndi Aroni amene anamusankha.+ Yesaya 63:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo anayamba kukumbukira masiku akale, masiku a Mose mtumiki wake, ndipo anafunsa kuti: “Kodi amene anawatulutsa m’nyanja+ pamodzi ndi abusa a anthu ake uja, ali kuti?+ Ali kuti amene anaika mzimu wake woyera mwa iye?+ Machitidwe 7:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ine ndaona ndithu mmene anthu anga amene ali ku Iguputo akuwazunzira.+ Ndamva kubuula kwawo+ ndipo ndatsika kudzawalanditsa.+ Tsopano tamvera. Ndikufuna ndikutume ku Iguputo.’+
6 Ndiyeno Samueli anauza anthuwo kuti: “Yehova ndiye mboni, iye amene anagwiritsa ntchito Mose ndi Aroni, amenenso anatulutsa makolo anu m’dziko la Iguputo.+
11 Iwo anayamba kukumbukira masiku akale, masiku a Mose mtumiki wake, ndipo anafunsa kuti: “Kodi amene anawatulutsa m’nyanja+ pamodzi ndi abusa a anthu ake uja, ali kuti?+ Ali kuti amene anaika mzimu wake woyera mwa iye?+
34 Ine ndaona ndithu mmene anthu anga amene ali ku Iguputo akuwazunzira.+ Ndamva kubuula kwawo+ ndipo ndatsika kudzawalanditsa.+ Tsopano tamvera. Ndikufuna ndikutume ku Iguputo.’+