Ekisodo 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Mose anauza Yehova kuti: “Pepani Yehova, ine sinditha kulankhula, kuyambira kalekale, kapena pamene mwalankhula ndi ine mtumiki wanu. Pakuti ndimalankhula movutikira ndipo ndine wa lilime lolemera.”+ Yeremiya 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma ine ndinati: “Haa! Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ine sindingathe kulankhula+ chifukwa ndine mwana.”+ Machitidwe 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chotero Mose anaphunzira nzeru+ zonse za Aiguputo. Ndipo anali wamphamvu m’mawu+ ndi m’zochita zake.
10 Ndiyeno Mose anauza Yehova kuti: “Pepani Yehova, ine sinditha kulankhula, kuyambira kalekale, kapena pamene mwalankhula ndi ine mtumiki wanu. Pakuti ndimalankhula movutikira ndipo ndine wa lilime lolemera.”+
6 Koma ine ndinati: “Haa! Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ine sindingathe kulankhula+ chifukwa ndine mwana.”+
22 Chotero Mose anaphunzira nzeru+ zonse za Aiguputo. Ndipo anali wamphamvu m’mawu+ ndi m’zochita zake.