Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 26:58
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 58 Nawa mabanja a Alevi: banja la Alibini,+ banja la Aheburoni,+ banja la Amali,+ banja la Amusi,+ ndi banja la Akora.+

      Kohati+ anabereka Amuramu.+

  • 1 Mbiri 9:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Panalinso Salumu mwana wa Kore. Kore anali mwana wa Ebiasafu+ ndipo Ebiasafu anali mwana+ wa Kora.+ Salumu ndi abale ake a nyumba ya makolo ake, Akora,+ anali oyang’anira ntchito pochita utumiki wawo pamodzi ndi makolo awo, monga alonda+ a pachihema pamsasa wa Yehova. Iwo anali alonda a pachipata.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena