Ekisodo 6:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndipo ana aamuna a Kora anali Asiri, Elikana ndi Abiasafu.+ Amenewa ndiwo anali mabanja a Kora.+ 1 Mbiri 6:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Awa ndiwo anali kutumikira, komanso ana awo: Pa ana a Akohati, Hemani+ woimba, mwana wa Yoweli.+ Yoweli anali mwana wa Samueli,+ 1 Mbiri 6:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Zefaniya anali mwana wa Tahati, Tahati anali mwana wa Asiri, Asiri anali mwana wa Ebiasafu,+ Ebiasafu anali mwana wa Kora,+
33 Awa ndiwo anali kutumikira, komanso ana awo: Pa ana a Akohati, Hemani+ woimba, mwana wa Yoweli.+ Yoweli anali mwana wa Samueli,+
37 Zefaniya anali mwana wa Tahati, Tahati anali mwana wa Asiri, Asiri anali mwana wa Ebiasafu,+ Ebiasafu anali mwana wa Kora,+