Ekisodo 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iyeyo ndiye azikalankhula kwa anthu m’malo mwa iwe.+ Choncho adzakhala ngati kamwa lako, ndipo iwe udzakhala ngati Mulungu kwa iye.+ Salimo 82:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Ine ndanena kuti, ‘Inu ndinu milungu,+Ndipo nonsenu ndinu ana a Wam’mwambamwamba.+
16 Iyeyo ndiye azikalankhula kwa anthu m’malo mwa iwe.+ Choncho adzakhala ngati kamwa lako, ndipo iwe udzakhala ngati Mulungu kwa iye.+