Salimo 78:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Anapereka zokolola zawo kwa mphemvu,Ndipo ntchito yawo yolemetsa anaipereka kwa dzombe.+ Salimo 105:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Analamula kuti pagwe dzombe,+Ndipo panagwa dzombe losawerengeka la mtundu winawake.+