Ekisodo 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pomwepo Mose analoza dziko lonse la Iguputo ndi ndodo yake, ndipo Yehova anachititsa mphepo yochokera kum’mawa+ kuwomba padziko lonselo, usana wonse ndi usiku wonse. M’mawa kutacha mphepoyo inabweretsa dzombe. Deuteronomo 28:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 “Udzapita ndi mbewu zambiri kumunda, koma udzakolola zochepa+ chifukwa dzombe lidzadya mbewuzo.+ Salimo 78:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Anapereka zokolola zawo kwa mphemvu,Ndipo ntchito yawo yolemetsa anaipereka kwa dzombe.+
13 Pomwepo Mose analoza dziko lonse la Iguputo ndi ndodo yake, ndipo Yehova anachititsa mphepo yochokera kum’mawa+ kuwomba padziko lonselo, usana wonse ndi usiku wonse. M’mawa kutacha mphepoyo inabweretsa dzombe.