Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 41:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Anaonanso ngala zina 7 zikutuluka pambuyo pa zoyambazo.+ Ngalazo zinali zonyala ndi zowauka ndi mphepo yakum’mawa.+

  • Ekisodo 14:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Tsopano Mose anatambasula dzanja lake kuloza panyanja,+ ndipo Yehova anachititsa mphepo yamphamvu yakum’mawa kuyamba kugawa nyanjayo usiku wonse ndi kuumitsa pansi pake.+ Motero madziwo anali kugawikana.+

  • Salimo 78:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Anachititsa mphepo ya kum’mawa kuwomba m’mlengalenga,+

      Ndipo mwa mphamvu zake anachititsa mphepo ya kum’mwera kuwomba.+

  • Yona 4:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Dzuwa litatuluka, Mulungu anatumiza mphepo yotentha yochokera kum’mawa.+ Dzuwalo linamutentha Yona pamutu moti anangotsala pang’ono kukomoka.+ Choncho Yona anapempha mobwerezabwereza kuti angofa. Iye anali kunena kuti: “Kuli bwino ndife kusiyana n’kuti ndikhale ndi moyo.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena