Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 7:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Koma ine ndidzamusiya Farao kuti aumitse mtima wake,+ ndipo ndidzachita zizindikiro ndi zozizwitsa zochuluka m’dziko la Iguputo.+

  • Ekisodo 11:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndipo Mose ndi Aroni anachita zozizwitsa zonsezi pamaso pa Farao.+ Koma Yehova analola Farao kuumitsa mtima wake, moti sanalole ana a Isiraeli kuchoka m’dziko lake.+

  • Yohane 12:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 “Wachititsa khungu maso awo ndipo waumitsa mitima yawo,+ kuti asamaone ndi maso awowo, asazindikire ndi mitima yawo ndi kutembenuka kuti ine ndiwachiritse.”+

  • Aroma 9:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Chotero, iye amachitira chifundo munthu amene wafuna kumuchitira chifundo,+ koma amalola anthu ena kuti aumitse mitima yawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena