Ekisodo 34:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Popereka magazi a nsembe yanga musawapereke limodzi ndi chilichonse chofufumitsa.+ Ndipo nsembe ya chikondwerero cha pasika isamagone mpaka m’mawa.+ Deuteronomo 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Uzipereka nsembe ya pasika kwa Yehova Mulungu wako.+ Uzipereka nkhosa ndi ng’ombe+ pamalo amene Yehova adzasankhe kuikapo dzina lake.+ 1 Akorinto 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chotsani chofufumitsa chakalecho, kuti mukhale mtanda watsopano,+ popeza ndinu opanda chofufumitsa. Pakuti Khristu+ waperekedwa+ monga nsembe yathu ya pasika.+
25 “Popereka magazi a nsembe yanga musawapereke limodzi ndi chilichonse chofufumitsa.+ Ndipo nsembe ya chikondwerero cha pasika isamagone mpaka m’mawa.+
2 Uzipereka nsembe ya pasika kwa Yehova Mulungu wako.+ Uzipereka nkhosa ndi ng’ombe+ pamalo amene Yehova adzasankhe kuikapo dzina lake.+
7 Chotsani chofufumitsa chakalecho, kuti mukhale mtanda watsopano,+ popeza ndinu opanda chofufumitsa. Pakuti Khristu+ waperekedwa+ monga nsembe yathu ya pasika.+