23 Ndiyeno Abulahamu anatenga mwana wake Isimaeli ndi amuna onse obadwira m’nyumba yake, ndi aliyense amene anamugula ndi ndalama zake, komanso mwamuna aliyense wa m’nyumba ya Abulahamu. Anawadula khungu lawo la kunsonga tsiku lomwelo, monga mmene Mulungu anamuuzira.+