Yoswa 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo, iwo anayamba kufuulira Yehova.+ Choncho ine ndinaika mdima pakati pa iwo ndi Aiguputuwo,+ ndipo ine ndinawamiza ndi madzi a m’nyanja.+ Munaona ndi maso anu zimene ndinachita ku Iguputo.+ Kenako, inu munakhala m’chipululu masiku ambiri.+ Nehemiya 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Choncho inu munaona+ nsautso ya makolo athu ku Iguputo ndipo munamvanso kulira kwawo pa Nyanja Yofiira.+ Salimo 34:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Olungama anafuula, ndipo Yehova anamva,+Iye anawapulumutsa m’masautso awo onse.+ Salimo 107:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iwo anapitiriza kufuulira Yehova m’masautso awo,+Ndipo anawalanditsa ku mavuto awo.+
7 Pamenepo, iwo anayamba kufuulira Yehova.+ Choncho ine ndinaika mdima pakati pa iwo ndi Aiguputuwo,+ ndipo ine ndinawamiza ndi madzi a m’nyanja.+ Munaona ndi maso anu zimene ndinachita ku Iguputo.+ Kenako, inu munakhala m’chipululu masiku ambiri.+
9 “Choncho inu munaona+ nsautso ya makolo athu ku Iguputo ndipo munamvanso kulira kwawo pa Nyanja Yofiira.+