2 Mafumu 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno Elisa anapita pamene panayambira madziwo n’kuponyapo mchere uja,+ n’kunena kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Ndakonza madziwa kuti akhale abwino.+ Sadzachititsanso imfa kapena kuchititsa akazi kupita padera.’”
21 Ndiyeno Elisa anapita pamene panayambira madziwo n’kuponyapo mchere uja,+ n’kunena kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Ndakonza madziwa kuti akhale abwino.+ Sadzachititsanso imfa kapena kuchititsa akazi kupita padera.’”