Ekisodo 15:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Zitatero Mose anafuulira Yehova+ ndipo Yehova anam’sonyeza kamtengo. Mose anaponya kamtengoko m’madzi moti madziwo anakhala okoma.+ Pamenepo Mulungu anawakhazikitsira lamulo ndi maziko operekera chiweruzo, ndipo pa nthawiyo anawayesa.+ 2 Mafumu 4:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndiyeno Elisa anati: “Bweretsani ufa.” Atathira ufawo mumphikamo, ananena kuti: “Apatseni anthuwa kuti adye.” Atatero, mumphikamo munalibenso chakupha chilichonse.+
25 Zitatero Mose anafuulira Yehova+ ndipo Yehova anam’sonyeza kamtengo. Mose anaponya kamtengoko m’madzi moti madziwo anakhala okoma.+ Pamenepo Mulungu anawakhazikitsira lamulo ndi maziko operekera chiweruzo, ndipo pa nthawiyo anawayesa.+
41 Ndiyeno Elisa anati: “Bweretsani ufa.” Atathira ufawo mumphikamo, ananena kuti: “Apatseni anthuwa kuti adye.” Atatero, mumphikamo munalibenso chakupha chilichonse.+