Ekisodo 15:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Zitatero Mose anafuulira Yehova+ ndipo Yehova anam’sonyeza kamtengo. Mose anaponya kamtengoko m’madzi moti madziwo anakhala okoma.+ Pamenepo Mulungu anawakhazikitsira lamulo ndi maziko operekera chiweruzo, ndipo pa nthawiyo anawayesa.+ 2 Mafumu 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno Elisa anapita pamene panayambira madziwo n’kuponyapo mchere uja,+ n’kunena kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Ndakonza madziwa kuti akhale abwino.+ Sadzachititsanso imfa kapena kuchititsa akazi kupita padera.’”
25 Zitatero Mose anafuulira Yehova+ ndipo Yehova anam’sonyeza kamtengo. Mose anaponya kamtengoko m’madzi moti madziwo anakhala okoma.+ Pamenepo Mulungu anawakhazikitsira lamulo ndi maziko operekera chiweruzo, ndipo pa nthawiyo anawayesa.+
21 Ndiyeno Elisa anapita pamene panayambira madziwo n’kuponyapo mchere uja,+ n’kunena kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Ndakonza madziwa kuti akhale abwino.+ Sadzachititsanso imfa kapena kuchititsa akazi kupita padera.’”