Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 1:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Choncho ndinatenga atsogoleri a mafuko anu, amuna anzeru ndi ozindikira n’kuwaika kukhala atsogoleri a magulu a anthu 1,000, atsogoleri a magulu a anthu 100, atsogoleri a magulu a anthu 50, atsogoleri a magulu a anthu 10, ndi akapitawo a m’mafuko anu.+

  • Machitidwe 14:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Komanso, anawaikira akulu+ mumpingo uliwonse, ndipo atapemphera ndi kusala kudya,+ anawapereka kwa Yehova+ yemwe anamukhulupirira.

  • Tito 1:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndinakusiya ku Kerete+ kuti ukonze zinthu zosalongosoka ndi kuti uike+ akulu mumzinda uliwonse, malinga ndi malangizo+ amene ndinakupatsa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena