Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 7:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ngati akupereka nsembeyo posonyeza kuyamikira,+ pamenepo azipereka nsembe yoyamikira pamodzi ndi mkate wozungulira woboola pakati, wopanda chofufumitsa, wothira mafuta. Aziperekanso timitanda ta mkate topyapyala topanda chofufumitsa, topaka mafuta,+ ndi mkate wozungulira woboola pakati, wothira mafuta, wophika ndi ufa wosalala wosakaniza bwino kwambiri ndi mafuta.

  • Salimo 107:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Iwo apereke nsembe zoyamikira,+

      Ndi kulengeza za ntchito zake ndi mfuu yachisangalalo.+

  • Salimo 116:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndidzapereka nsembe zoyamikira kwa inu,+

      Ndipo ndidzaitana pa dzina la Yehova.+

  • Amosi 4:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Perekani nsembe zoyamikira zautsi kuchokera pa zinthu zokhala ndi chofufumitsa+ ndipo lengezani ndi kufalitsa za nsembe zaufulu+ pakuti ndi zimene mukukonda, inu ana a Isiraeli,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena