Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 7:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ngati akupereka nsembeyo posonyeza kuyamikira,+ pamenepo azipereka nsembe yoyamikira pamodzi ndi mkate wozungulira woboola pakati, wopanda chofufumitsa, wothira mafuta. Aziperekanso timitanda ta mkate topyapyala topanda chofufumitsa, topaka mafuta,+ ndi mkate wozungulira woboola pakati, wothira mafuta, wophika ndi ufa wosalala wosakaniza bwino kwambiri ndi mafuta.

  • Salimo 50:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Amene akupereka nsembe yoyamikira kwa ine ndi amene akundilemekeza.+

      Ndipo amene akuyenda panjirayo motsimikiza,

      Ndidzamuonetsa chipulumutso changa.”+

  • Salimo 107:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Iwo apereke nsembe zoyamikira,+

      Ndi kulengeza za ntchito zake ndi mfuu yachisangalalo.+

  • Aheberi 13:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kudzera mwa iye, tiyeni nthawi zonse tizitamanda Mulungu. Tizichita zimenezi monga nsembe imene tikupereka kwa Mulungu,+ yomwe ndi chipatso cha milomo yathu.+ Timagwiritsa ntchito milomo imeneyi polengeza dzina lake kwa anthu ena.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena