Levitiko 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Popereka nsembe zachiyanjano, zimene ndi nsembe yoyamikira pamodzi ndi nsembe yake ya mkate, aziperekanso makeke okhala ndi chofufumitsa,+ ozungulira oboola pakati. Aroma 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiye chifukwa chake monga mmene uchimo unalowera m’dziko kudzera mwa munthu mmodzi,+ ndi imfa+ kudzera mwa uchimo, imfayo n’kufalikira kwa anthu onse chifukwa onse anachimwa+ . . .
13 Popereka nsembe zachiyanjano, zimene ndi nsembe yoyamikira pamodzi ndi nsembe yake ya mkate, aziperekanso makeke okhala ndi chofufumitsa,+ ozungulira oboola pakati.
12 Ndiye chifukwa chake monga mmene uchimo unalowera m’dziko kudzera mwa munthu mmodzi,+ ndi imfa+ kudzera mwa uchimo, imfayo n’kufalikira kwa anthu onse chifukwa onse anachimwa+ . . .