Levitiko 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘Nsembe yambewu imene mudzapereka kwa Yehova ikhale yopanda chofufumitsa,+ chifukwa simuyenera kutentha mtanda wofufumitsa wa ufa wokanda ndiponso uchi,* monga nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova. Levitiko 23:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Muzibweretsa mitanda iwiri ya mkate+ wa m’nyumba mwanu kuti ikhale nsembe yoweyula. Mitandayo izikhala yopangidwa ndi ufa wosalala wokwanira magawo awiri mwa magawo 10 a muyezo wa efa. Poiphika izikhala ndi chofufumitsa,+ ndipo muziipereka kwa Yehova monga zipatso zoyambirira kucha.+
11 “‘Nsembe yambewu imene mudzapereka kwa Yehova ikhale yopanda chofufumitsa,+ chifukwa simuyenera kutentha mtanda wofufumitsa wa ufa wokanda ndiponso uchi,* monga nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova.
17 Muzibweretsa mitanda iwiri ya mkate+ wa m’nyumba mwanu kuti ikhale nsembe yoweyula. Mitandayo izikhala yopangidwa ndi ufa wosalala wokwanira magawo awiri mwa magawo 10 a muyezo wa efa. Poiphika izikhala ndi chofufumitsa,+ ndipo muziipereka kwa Yehova monga zipatso zoyambirira kucha.+