Yeremiya 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Afesa tirigu koma akolola minga.+ Agwira ntchito mpaka kudwala nayo, koma osapeza phindu lililonse.+ Iwo adzachita manyazi ndi zokolola zawo chifukwa mkwiyo waukulu wa Yehova udzawayakira.” Hagai 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwafesa mbewu zambiri koma zokolola zanu n’zochepa.+ Mukudya koma simukukhuta.+ Mukumwa koma simukukhutira.* Mukuvala zovala koma simukumva kutentha. Amene akugwira ganyu akulandirira ndalama zake m’matumba obowoka.’”+
13 Afesa tirigu koma akolola minga.+ Agwira ntchito mpaka kudwala nayo, koma osapeza phindu lililonse.+ Iwo adzachita manyazi ndi zokolola zawo chifukwa mkwiyo waukulu wa Yehova udzawayakira.”
6 Mwafesa mbewu zambiri koma zokolola zanu n’zochepa.+ Mukudya koma simukukhuta.+ Mukumwa koma simukukhutira.* Mukuvala zovala koma simukumva kutentha. Amene akugwira ganyu akulandirira ndalama zake m’matumba obowoka.’”+