Genesis 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako, Yehova Mulungu anaumba munthu kuchokera kufumbi lapansi,+ ndipo anauzira mpweya wa moyo+ m’mphuno mwake, munthuyo n’kukhala wamoyo.+ Genesis 46:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ana onse a Yakobo otuluka m’chiuno mwake,+ amene anali nawo ku Iguputo, analipo 66 onse pamodzi, osawerengera akazi a ana ake. Ezekieli 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamverani! Miyoyo yonse ndi yanga.+ Moyo+ wa bambo komanso moyo wa mwana, yonse ndi yanga.+ Moyo umene ukuchimwawo+ ndi umene udzafe.+
7 Kenako, Yehova Mulungu anaumba munthu kuchokera kufumbi lapansi,+ ndipo anauzira mpweya wa moyo+ m’mphuno mwake, munthuyo n’kukhala wamoyo.+
26 Ana onse a Yakobo otuluka m’chiuno mwake,+ amene anali nawo ku Iguputo, analipo 66 onse pamodzi, osawerengera akazi a ana ake.
4 Tamverani! Miyoyo yonse ndi yanga.+ Moyo+ wa bambo komanso moyo wa mwana, yonse ndi yanga.+ Moyo umene ukuchimwawo+ ndi umene udzafe.+