Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 29:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Popereka mwana wa nkhosa woyamba, uzipereka limodzi ndi ufa wosalala,+ muyezo wake gawo limodzi mwa magawo 10 a muyezo wa efa,* wothira mafuta oyenga bwino kwambiri okwana gawo limodzi mwa magawo anayi a muyezo wa hini,* ndi gawo limodzi mwa magawo anayi a vinyo wa nsembe yachakumwa.+

  • Levitiko 2:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “‘Munthu akafuna kupereka nsembe yambewu+ kwa Yehova, nsembe yakeyo izikhala ufa wosalala.+ Azithira mafuta ndi kuika lubani* pa ufawo.

  • Levitiko 9:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Kenako anapereka nsembe yambewu.+ Anatapako nsembeyo kudzaza dzanja lake ndi kuitentha paguwa lansembe, kuwonjezera pa nsembe yopsereza ya m’mawa.+

  • Numeri 28:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Muzipereka nsembezi limodzi ndi ufa wosalala wokwana gawo limodzi mwa magawo 10 a muyezo wa efa,+ monga nsembe yambewu.+ Ufawo muziuthira mafuta oyenga bwino kwambiri okwana gawo limodzi mwa magawo anayi a muyezo wa hini.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena