Genesis 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Yehova Mulungu anauza njokayo+ kuti: “Chifukwa cha zimene wachitazi, ukhala wotembereredwa pa nyama zonse zoweta ndi zakutchire. Udzakwawa ndi mimba yako ndipo udzadya fumbi masiku onse a moyo wako.+ Mika 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Adzanyambita fumbi ngati njoka.+ Adzatuluka m’malo awo obisalamo+ ngati zokwawa zapadziko lapansi ali ndi mantha. Adzabwera kwa Yehova Mulungu akunjenjemera ndipo adzachita nanu mantha.”+
14 Tsopano Yehova Mulungu anauza njokayo+ kuti: “Chifukwa cha zimene wachitazi, ukhala wotembereredwa pa nyama zonse zoweta ndi zakutchire. Udzakwawa ndi mimba yako ndipo udzadya fumbi masiku onse a moyo wako.+
17 Adzanyambita fumbi ngati njoka.+ Adzatuluka m’malo awo obisalamo+ ngati zokwawa zapadziko lapansi ali ndi mantha. Adzabwera kwa Yehova Mulungu akunjenjemera ndipo adzachita nanu mantha.”+