Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 12:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kenako mtambo uja unachoka pamwamba pa chihemacho. Pomwepo, Miriamu anagwidwa ndi khate loyera mbuu!+ Aroni atacheuka, anangoona kuti Miriamu wachita khate.+

  • 2 Mbiri 26:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Koma Uziya anakwiya kwambiri+ atanyamula chiwaya chofukizira+ m’manja mwake. Atawakwiyira choncho ansembewo, khate+ linabuka+ pamphumi pake ali pamaso pa ansembewo m’nyumba ya Yehova pambali pa guwa lansembe zofukiza.

  • Mateyu 8:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pamenepo Yesu anatambasula dzanja lake n’kumukhudza, ndipo anati: “Ndikufuna. Khala woyera.”+ Nthawi yomweyo khate lakelo linatha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena