Ezekieli 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Uuse moyo mosatulutsa mawu. Anthu akufa usawalire maliro.+ Uvale chovala chakumutu+ ndipo uvale nsapato zako.+ Usaphimbe ndevu zako zapamlomo,+ ndipo usadye chakudya chimene anthu angakupatse.”+ Mika 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Oona masomphenya+ adzachita manyazi+ ndipo olosera+ adzakhumudwa ndithu. Onsewa adzaphimba ndevu zawo zapamlomo+ chifukwa Mulungu sadzawayankha.’”+
17 Uuse moyo mosatulutsa mawu. Anthu akufa usawalire maliro.+ Uvale chovala chakumutu+ ndipo uvale nsapato zako.+ Usaphimbe ndevu zako zapamlomo,+ ndipo usadye chakudya chimene anthu angakupatse.”+
7 Oona masomphenya+ adzachita manyazi+ ndipo olosera+ adzakhumudwa ndithu. Onsewa adzaphimba ndevu zawo zapamlomo+ chifukwa Mulungu sadzawayankha.’”+