Yeremiya 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Yehova wanena kuti, ‘Usalowe m’nyumba imene olira maliro akuchitiramo phwando, ndipo usapite kukalira nawo maliro kapena kuwamvera chisoni.’+ “‘Pakuti anthu awa ndawachotsera mtendere wanga, kukoma mtima kosatha ndi chifundo,’+ watero Yehova.
5 “Yehova wanena kuti, ‘Usalowe m’nyumba imene olira maliro akuchitiramo phwando, ndipo usapite kukalira nawo maliro kapena kuwamvera chisoni.’+ “‘Pakuti anthu awa ndawachotsera mtendere wanga, kukoma mtima kosatha ndi chifundo,’+ watero Yehova.