3 Ndipo zotsala za nsembe yambewu ndi za Aroni ndi ana ake,+ popeza ndi zopatulika koposa,+ zochokera pansembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova.
7 Nsembe ya kupalamula ndi yofanana ndi nsembe yamachimo. Zonsezi lamulo lake ndi limodzi.+ Nyama ya nsembe yophimba machimo izikhala ya wansembe amene wapereka nsembeyo.