Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 3:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pamenepo azipereka mbali ina ya nsembe yachiyanjanoyo monga nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova. Azipereka mafuta+ okuta matumbo, mafuta onse amene ali pamatumbo.+

  • Levitiko 3:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndipo pansembe yachiyanjanoyo azitengapo mafuta ake ndi kuwapereka kwa Yehova monga nsembe yotentha ndi moto.+ Azichotsa mchira wonse wamafuta+ pafupi ndi fupa la msana ndiponso mafuta okuta matumbo, mafuta onse amene ali pamatumbo.+

  • Levitiko 4:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Mafuta onse a mbuziyo aziwatentha paguwa lansembe mofanana ndi mafuta a nsembe yachiyanjano.+ Pamenepo wansembe aziphimba tchimo la mtsogoleriyo,+ ndipo azikhululukidwa.

  • Salimo 20:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Akumbukire nsembe zanu zonse zimene munapereka monga mphatso.+

      Alandire mafuta a nsembe zanu zopsereza.+ [Seʹlah.]

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena