Levitiko 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno aziika dzanja lake pamutu+ pa ng’ombeyo, ndipo aziipha pakhomo la chihema chokumanako. Akatero ana a Aroni, ansembe, aziwaza magazi ake mozungulira paguwa lansembe. Levitiko 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘Tsopano lamulo la nsembe yachiyanjano+ imene aliyense azipereka kwa Yehova lili motere:
2 Ndiyeno aziika dzanja lake pamutu+ pa ng’ombeyo, ndipo aziipha pakhomo la chihema chokumanako. Akatero ana a Aroni, ansembe, aziwaza magazi ake mozungulira paguwa lansembe.