3 Ine ndidzam’kana* munthu ameneyo, ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake,+ chifukwa wapereka mwana wake kwa Moleki kuti aipitse malo anga oyera+ ndi kuipitsa dzina langa loyera.+
20 Pamenepo iwo anapita kwa anthu a mitundu ina ndipo anthuwo anayamba kudetsa dzina langa loyera+ ponena za iwowo kuti, ‘Awa ndi anthu a Yehova, ndipo anachoka m’dziko lake.’+