Levitiko 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Ngati akupereka ng’ombe kuti ikhale nsembe yake yopsereza,+ azipereka yamphongo, yopanda chilema.+ Aziipereka kwa Yehova mwa kufuna kwake,+ pakhomo la chihema chokumanako. Levitiko 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Uza Aroni ndi ana ake kuti, ‘Lamulo la nsembe yamachimo+ lili motere: Nyama ya nsembe yamachimo iziphedwa pamaso pa Yehova, pamalo+ ophera nyama ya nsembe yopsereza nthawi zonse. Chimenechi ndi chinthu chopatulika koposa.+
3 “‘Ngati akupereka ng’ombe kuti ikhale nsembe yake yopsereza,+ azipereka yamphongo, yopanda chilema.+ Aziipereka kwa Yehova mwa kufuna kwake,+ pakhomo la chihema chokumanako.
25 “Uza Aroni ndi ana ake kuti, ‘Lamulo la nsembe yamachimo+ lili motere: Nyama ya nsembe yamachimo iziphedwa pamaso pa Yehova, pamalo+ ophera nyama ya nsembe yopsereza nthawi zonse. Chimenechi ndi chinthu chopatulika koposa.+