Levitiko 18:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Motero inu muzisunga mfundo zanga ndi zigamulo zanga.+ Ndipo aliyense wa inu, kaya ndi nzika kapena mlendo wokhala pakati panu,+ musachite chilichonse cha zinthu zonyansa zimenezi. Salimo 105:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Anachita zimenezi kuti asunge malangizo ake,+Ndi kusunga malamulo ake.+Tamandani Ya, anthu inu!+ Salimo 119:80 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 80 Mtima wanga usunge malangizo anu mosalakwitsa kanthu,+Kuti ndisachite manyazi.+ Mlaliki 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Poti zonse zanenedwa, mfundo yaikulu ndi yakuti: Opa Mulungu woona+ ndi kusunga malamulo ake+ chifukwa zimenezi ndiye zimene munthu ayenera kuchita.
26 Motero inu muzisunga mfundo zanga ndi zigamulo zanga.+ Ndipo aliyense wa inu, kaya ndi nzika kapena mlendo wokhala pakati panu,+ musachite chilichonse cha zinthu zonyansa zimenezi.
13 Poti zonse zanenedwa, mfundo yaikulu ndi yakuti: Opa Mulungu woona+ ndi kusunga malamulo ake+ chifukwa zimenezi ndiye zimene munthu ayenera kuchita.