Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 19:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Munthu aliyense wokhudza mtembo, thupi la munthu aliyense amene angamwalire, amene sadzadziyeretsa, adzaipitsa chihema cha Yehova.+ Munthu ameneyo aphedwe kuti asakhalenso pakati pa Isiraeli.+ Iye ndi wodetsedwa chifukwa sanawazidwe madzi oyeretsera.+ Chidetso chake chikadali pa iye.+

  • Numeri 19:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 “‘Limeneli likhale lamulo mpaka kalekale kwa iwo, kuti munthu wowaza madzi oyeretsera, komanso munthu amene angakhudze madziwo, azichapa zovala zake.+ Akatero, azikhalabe wodetsedwa mpaka madzulo.

  • Numeri 31:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 chilichonse chimene sichingapse ndi moto,+ chidutse pamoto kuti chikhale choyera. Muchiyeretsenso ndi madzi.+ Koma chilichonse chimene chingapse ndi moto muchiyeretse ndi madzi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena