Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 12:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Odalitsa iwe ndidzawadalitsa, ndipo otemberera iwe ndidzawatemberera.+ Mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso* chifukwa cha iwe.”+

  • Numeri 23:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Pamenepo Balamu anayamba kulankhula mwa ndakatulo,+ kuti:

      “Balaki mfumu ya Mowabu yandiitana kuchokera ku Aramu,+

      Kuchokera kumapiri a kum’mawa, kuti:

      ‘Bwera, udzanditembererere Yakobo.

      Bwera, udzaitanire tsoka pa Isiraeli.’+

  • Yoswa 24:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Kenako Balaki mwana wa Zipori,+ mfumu ya Mowabu, ananyamuka kukamenyana ndi Isiraeli.+ Iye anaitanitsa Balamu, mwana wa Beori, ndi kumuuza kuti akutemberereni.+

  • Nehemiya 13:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 chifukwa iwowa sanachingamire ana a Isiraeli kuti awapatse chakudya+ ndi madzi.+ M’malomwake, analemba ganyu Balamu+ kuti awatemberere.+ Koma Mulungu wathu anasintha temberero limenelo kukhala dalitso.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena