Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 14:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 N’chifukwa chake mzinda wa Heburoni uli cholowa cha Kalebe mwana wa Yefune Mkenizi, kufikira lero. Anam’patsa mzindawo chifukwa iye anatsatira Yehova Mulungu wa Isiraeli ndi mtima wake wonse.+

  • Yesaya 26:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 “Anthu anu amene anafa adzakhalanso ndi moyo.+ Anthu anga amene anafa adzadzuka ndi kuimirira.+ Inu anthu okhala m’fumbi, dzukani, fuulani mokondwera!+ Pakuti mame anu+ ali ngati mame a maluwa,+ ndipo dziko lapansi lidzabereka anthu amene anafa.+

  • 1 Akorinto 15:55
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 55 “Imfa iwe, kupambana kwako kuli kuti? Imfawe, mphamvu yako ili kuti?”+

  • Aheberi 11:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Akazi analandira akufa awo amene anauka kwa akufa.+ Koma anthu ena anazunzidwa chifukwa sanalole kusiya chikhulupiriro chawo kuti amasulidwe. Iwo anachita zimenezi kuti adzauke kwa akufa, komwe ndi kuuka kwabwino kwambiri.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena