Numeri 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Upange malipenga+ awiri asiliva. Uchite kusula, ndipo uziwagwiritsa ntchito poitanitsa+ msonkhano ndi posamutsa msasa. Numeri 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Adani okuvutitsani akakuukirani+ kuti akuthireni nkhondo m’dziko lanu, muziliza malipengawo+ moitanira asilikali kunkhondo. Mukatero, Mulungu wanu Yehova adzakukumbukirani ndithu ndi kukupulumutsani kwa adani anuwo.+
2 “Upange malipenga+ awiri asiliva. Uchite kusula, ndipo uziwagwiritsa ntchito poitanitsa+ msonkhano ndi posamutsa msasa.
9 “Adani okuvutitsani akakuukirani+ kuti akuthireni nkhondo m’dziko lanu, muziliza malipengawo+ moitanira asilikali kunkhondo. Mukatero, Mulungu wanu Yehova adzakukumbukirani ndithu ndi kukupulumutsani kwa adani anuwo.+