Genesis 19:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 M’kupita kwa nthawi, mwana woyambayo anabereka mwana wamwamuna n’kumutcha dzina lakuti Mowabu.+ Iye ndiye tate wa Amowabu mpaka lero.+ Numeri 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako anasamuka ku Oboti n’kukamanga msasa ku Iye-abarimu,+ m’chipululu choyang’anana ndi dziko la Mowabu, kotulukira dzuwa. Numeri 21:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Atasamuka kumeneko anakamanga msasa m’dera la chigwa cha Arinoni,+ m’chipululu chochokera kumalire a dziko la Aamori. Chigwa cha Arinoni chinali malire pakati pa dziko la Mowabu ndi la Aamori.
37 M’kupita kwa nthawi, mwana woyambayo anabereka mwana wamwamuna n’kumutcha dzina lakuti Mowabu.+ Iye ndiye tate wa Amowabu mpaka lero.+
11 Kenako anasamuka ku Oboti n’kukamanga msasa ku Iye-abarimu,+ m’chipululu choyang’anana ndi dziko la Mowabu, kotulukira dzuwa.
13 Atasamuka kumeneko anakamanga msasa m’dera la chigwa cha Arinoni,+ m’chipululu chochokera kumalire a dziko la Aamori. Chigwa cha Arinoni chinali malire pakati pa dziko la Mowabu ndi la Aamori.