Oweruza 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ana a Benjamini sanapitikitse Ayebusi amene anali kukhala m’Yerusalemu,+ moti Ayebusiwo akukhalabe ndi ana a Benjamini m’Yerusalemu kufikira lero.+ Salimo 106:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Iwowa sanawononge mitundu ina ya anthu,+Mmene Yehova anawauzira.+
21 Ana a Benjamini sanapitikitse Ayebusi amene anali kukhala m’Yerusalemu,+ moti Ayebusiwo akukhalabe ndi ana a Benjamini m’Yerusalemu kufikira lero.+