Numeri 14:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma mwa amuna amene anakazonda dzikolo, Yoswa mwana wa Nuni ndi Kalebe mwana wa Yefune, adzakhalabe ndi moyo ndithu.”’”+ Numeri 27:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chotero Yehova anauza Mose kuti: “Tenga Yoswa mwana wa Nuni, munthu wolimba mtima,*+ ndipo uike manja ako pa iye.+
38 Koma mwa amuna amene anakazonda dzikolo, Yoswa mwana wa Nuni ndi Kalebe mwana wa Yefune, adzakhalabe ndi moyo ndithu.”’”+
18 Chotero Yehova anauza Mose kuti: “Tenga Yoswa mwana wa Nuni, munthu wolimba mtima,*+ ndipo uike manja ako pa iye.+