Ekisodo 30:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndiyeno Yehova anapitiriza kulankhula ndi Mose kuti: “Tenga zonunkhira izi:+ madontho a sitakate,* onika, mafuta onunkhira a galibanamu ndi lubani*+ weniweni. Zonsezi zikhale za muyezo wofanana. Deuteronomo 33:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Amenewa azilangiza Yakobo pa zigamulo zanu,+Ndi Isiraeli m’chilamulo chanu.+Azipereka nsembe zofukiza kuti muzinunkhiza fungo lake,+Ndi nsembe yathunthu paguwa lanu lansembe.+
34 Ndiyeno Yehova anapitiriza kulankhula ndi Mose kuti: “Tenga zonunkhira izi:+ madontho a sitakate,* onika, mafuta onunkhira a galibanamu ndi lubani*+ weniweni. Zonsezi zikhale za muyezo wofanana.
10 Amenewa azilangiza Yakobo pa zigamulo zanu,+Ndi Isiraeli m’chilamulo chanu.+Azipereka nsembe zofukiza kuti muzinunkhiza fungo lake,+Ndi nsembe yathunthu paguwa lanu lansembe.+