Levitiko 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Ngati akupereka ng’ombe kuti ikhale nsembe yake yopsereza,+ azipereka yamphongo, yopanda chilema.+ Aziipereka kwa Yehova mwa kufuna kwake,+ pakhomo la chihema chokumanako. Salimo 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Akumbukire nsembe zanu zonse zimene munapereka monga mphatso.+Alandire mafuta a nsembe zanu zopsereza.+ [Seʹlah.]
3 “‘Ngati akupereka ng’ombe kuti ikhale nsembe yake yopsereza,+ azipereka yamphongo, yopanda chilema.+ Aziipereka kwa Yehova mwa kufuna kwake,+ pakhomo la chihema chokumanako.
3 Akumbukire nsembe zanu zonse zimene munapereka monga mphatso.+Alandire mafuta a nsembe zanu zopsereza.+ [Seʹlah.]