Numeri 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano anthuwo anayamba kudandaula pamaso pa Yehova ngati kuti anali pamavuto.+ Yehova atamva kudandaulako anawapsera mtima, ndipo moto wa Yehova unawayakira n’kupsereza ena a iwo kumalire a msasa.+ Deuteronomo 32:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti pa kukwiya kwanga moto wayaka,+Ndipo udzayaka mpaka kukafika ku Manda,* malo a pansi penipeni.+Udzanyeketsa dziko lapansi ndi zipatso zake,+Ndi kuyatsa maziko a mapiri.+ Salimo 78:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho Yehova anamva zimenezo ndipo anakwiya.+Moti moto unayakira Yakobo,+Ndipo mkwiyo unatsikira pa Isiraeli.+
11 Tsopano anthuwo anayamba kudandaula pamaso pa Yehova ngati kuti anali pamavuto.+ Yehova atamva kudandaulako anawapsera mtima, ndipo moto wa Yehova unawayakira n’kupsereza ena a iwo kumalire a msasa.+
22 Pakuti pa kukwiya kwanga moto wayaka,+Ndipo udzayaka mpaka kukafika ku Manda,* malo a pansi penipeni.+Udzanyeketsa dziko lapansi ndi zipatso zake,+Ndi kuyatsa maziko a mapiri.+
21 Choncho Yehova anamva zimenezo ndipo anakwiya.+Moti moto unayakira Yakobo,+Ndipo mkwiyo unatsikira pa Isiraeli.+