Genesis 29:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Leya anakhalanso ndi pakati n’kubereka mwana wamwamuna, ndipo anati: “Yehova wandipatsa mwana wina chifukwa wandimvera+ kuti sindikukondedwa kwenikweni.” Choncho mwanayo anamutcha Simiyoni.*+ Genesis 49:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Simiyoni ndi Levi m’pachibale pawo.+ Malupanga awo ndiwo zida zochitira zachiwawa.+
33 Leya anakhalanso ndi pakati n’kubereka mwana wamwamuna, ndipo anati: “Yehova wandipatsa mwana wina chifukwa wandimvera+ kuti sindikukondedwa kwenikweni.” Choncho mwanayo anamutcha Simiyoni.*+