Numeri 31:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma Mose anakwiya nawo kwambiri atsogoleri a nkhondowo,+ atsogoleri a magulu a asilikali 1,000, ndi atsogoleri a magulu a asilikali 100, amene anachokera kunkhondo. Deuteronomo 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Mudziikire oweruza+ ndi atsogoleri+ m’mizinda yanu yonse imene Yehova Mulungu wanu akukupatsani, malinga ndi mafuko anu. Oweruza ndi atsogoleriwo aziweruza anthu ndi chiweruzo cholungama.
14 Koma Mose anakwiya nawo kwambiri atsogoleri a nkhondowo,+ atsogoleri a magulu a asilikali 1,000, ndi atsogoleri a magulu a asilikali 100, amene anachokera kunkhondo.
18 “Mudziikire oweruza+ ndi atsogoleri+ m’mizinda yanu yonse imene Yehova Mulungu wanu akukupatsani, malinga ndi mafuko anu. Oweruza ndi atsogoleriwo aziweruza anthu ndi chiweruzo cholungama.