Genesis 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ndi Ahori+ kuphiri lawo la Seiri,+ mpaka kukafika ku Eli-parana,+ kuchipululu. Genesis 36:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Nawa ana a Seiri Mhori, eni dzikolo:+ Lotani, Sobala, Zibeoni, Ana,+ Deuteronomo 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kale Ahori+ anali kukhala m’Seiri, ndipo ana a Esau+ anawalanda dzikolo ndi kuwapha. Atatero, ana a Esauwo anayamba kukhala m’dzikolo,+ monga mmene ana a Isiraeli ayenera kuchitira m’dziko lawo, limene Yehova adzawapatsa ndithu.)
12 Kale Ahori+ anali kukhala m’Seiri, ndipo ana a Esau+ anawalanda dzikolo ndi kuwapha. Atatero, ana a Esauwo anayamba kukhala m’dzikolo,+ monga mmene ana a Isiraeli ayenera kuchitira m’dziko lawo, limene Yehova adzawapatsa ndithu.)