Yeremiya 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “‘Pitani ku Silo,+ kumalo kumene poyamba kunali dzina langa,+ ndipo mukaone zimene ndinachitira malowo chifukwa cha kuipa kwa anthu anga Aisiraeli.+ Yeremiya 26:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 pamenepo ine ndidzachititsa nyumba iyi kukhala ngati nyumba ya ku Silo.+ Ndipo mzinda uwu ndidzausandutsa chinthu chotembereredwa pakati pa anthu a mitundu yonse ya padziko lapansi.’”’”+ Maliro 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Amene anali ndi anthu ambiri+ tsopano wakhala wopanda anthu.+Amene anali ndi anthu ambiri pakati pa mitundu ina+ wakhala ngati mkazi wamasiye.+Amene anali wolemekezeka pakati pa zigawo zina wayamba kugwira ntchito yaukapolo.+
12 “‘Pitani ku Silo,+ kumalo kumene poyamba kunali dzina langa,+ ndipo mukaone zimene ndinachitira malowo chifukwa cha kuipa kwa anthu anga Aisiraeli.+
6 pamenepo ine ndidzachititsa nyumba iyi kukhala ngati nyumba ya ku Silo.+ Ndipo mzinda uwu ndidzausandutsa chinthu chotembereredwa pakati pa anthu a mitundu yonse ya padziko lapansi.’”’”+
1 Amene anali ndi anthu ambiri+ tsopano wakhala wopanda anthu.+Amene anali ndi anthu ambiri pakati pa mitundu ina+ wakhala ngati mkazi wamasiye.+Amene anali wolemekezeka pakati pa zigawo zina wayamba kugwira ntchito yaukapolo.+