Nehemiya 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno munaonetsa Farao zizindikiro ndi zozizwitsa zomukhaulitsa pamodzi ndi atumiki ake onse ndi anthu onse okhala m’dziko lake.+ Munatero chifukwa munadziwa kuti iwo anachita zinthu modzikuza+ kwa makolo athu. Pamenepo munadzipangira dzina+ kufikira lero. Salimo 78:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Iwo sanakumbukire mmene anaikira zizindikiro zake mu Iguputo,+Ndi zozizwitsa zimene anachita m’dera la Zowani,+ Salimo 105:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iwowa anasonyeza Aiguputo zizindikiro za Mulungu,+Ndi zozizwitsa m’dziko la Hamu.+
10 Ndiyeno munaonetsa Farao zizindikiro ndi zozizwitsa zomukhaulitsa pamodzi ndi atumiki ake onse ndi anthu onse okhala m’dziko lake.+ Munatero chifukwa munadziwa kuti iwo anachita zinthu modzikuza+ kwa makolo athu. Pamenepo munadzipangira dzina+ kufikira lero.
43 Iwo sanakumbukire mmene anaikira zizindikiro zake mu Iguputo,+Ndi zozizwitsa zimene anachita m’dera la Zowani,+ Salimo 105:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iwowa anasonyeza Aiguputo zizindikiro za Mulungu,+Ndi zozizwitsa m’dziko la Hamu.+