Deuteronomo 11:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 dalitsoli mudzalilandira malinga ngati mudzamvera malamulo a Yehova Mulungu wanu,+ omwe ndikukupatsani lero, Deuteronomo 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Madalitso onsewa adzakutsata ndi kukupeza+ chifukwa ukumvera mawu a Yehova Mulungu wako:
27 dalitsoli mudzalilandira malinga ngati mudzamvera malamulo a Yehova Mulungu wanu,+ omwe ndikukupatsani lero,